BrainWave Media

BrainWave Media | Seeing Genius in every Brainwave 🧠 |
For Business,Promo and Adverts
+265 999017065

With Ashraf Omar Official – I'm on a streak! I've been a top fan for 4 months in a row. πŸŽ‰
06/09/2026

With Ashraf Omar Official – I'm on a streak! I've been a top fan for 4 months in a row. πŸŽ‰

Kodi inuo zabwino ayi? kapena nyimbo zokhala Ndima advert atatu otsogozana  zija zimakusangalatsani.Mukudizwa kuti ndi k...
27/08/2026

Kodi inuo zabwino ayi? kapena nyimbo zokhala Ndima advert atatu otsogozana zija zimakusangalatsani.
Mukudizwa kuti ndi k3,500 yokha m***a kumvera Sound popanda zima advert pa Spotify?
M***a kulipira through Airtel money or National bank, zonsezi ndi Tigule MarketPlace . Link mu comment section πŸ‘‡πŸ‘‡

22/08/2026

Fada amenewa anaiponda kwambiri mpaka kukanika kumenya turn then nkukaziombetsa nkutchoka nsana. πŸ˜‚
Iyitu inali practice yothamanga kukonzekera Mpikisano wa Olympic ku China. Apa zavuta ndizokaikitsa kuti angatengenso gawo mu mipikisanowu.

Telegram ikufuna kuti izigwiritsa ntchito domain yotchedwa  .gram. Ngati izi  zingavomerezedwa ndi ICANN, ogwiritsa ntch...
21/08/2026

Telegram ikufuna kuti izigwiritsa ntchito domain yotchedwa .gram. Ngati izi zingavomerezedwa ndi ICANN, ogwiritsa ntchito a telegram akhoza kupeza ma domain awoawo a .gram komanso kupanga ma website connected ndi Telegram.
Meanwhile, Instagram: πŸ₯²

Shine with beautiful pictures at affordable prices. Try awa graphic lab._weddings_engagements_birthday parties_indoor an...
20/08/2026

Shine with beautiful pictures at affordable prices. Try awa graphic lab.
_weddings
_engagements
_birthday parties
_indoor and outdoor pictures
Keep your memories with us.

14/08/2026

Dziko ili πŸ’”

Anthu simukuyankhula bwino eeish πŸ˜‚
11/08/2026

Anthu simukuyankhula bwino eeish πŸ˜‚

10/08/2026

Munamvapo za confirmation bias?

09/08/2026

Pakufunika page Yogulitsa 10k+ followers. Ngati ilipo bwerani ku whatsapp ndi mtengo.

04/08/2026

Zilibwino tsopano;
Usiku wabwino

Address

Capetown
Lilongwe

Telephone

+265995371612

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when BrainWave Media posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to BrainWave Media:

Shortcuts

Share