Chipa Tech

Chipa Tech It is a technological solutions providing company. CHIPA TECH was established in 2013

another Cohort done.Learn I.C.T  from us
11/03/2026

another Cohort done.
Learn I.C.T from us

teachers wanted
01/01/2026

teachers wanted

Ife Tikhala uku nanga inu mkutani.OSAYIWALA AND AKU MZUZU NDI MADELA OZUNGULILA TIKHALA NDIMAPHUZILO A COMPUTER AND PHON...
29/12/2025

Ife Tikhala uku nanga inu mkutani.
OSAYIWALA AND AKU MZUZU NDI MADELA OZUNGULILA

TIKHALA NDIMAPHUZILO A COMPUTER AND PHONE REPAIRING KUYAMBIRA PA 5 JANUARY 2026 ,NDIPO A WEEKEND AZAYAMBA PA 10 JANUARY 2026,
FEES NDI MK120,000 NDIPO AMENE AZATENGE MAPHUZIRO ONSE FEES IZAKHALA 100,000 PER PROGRAM,
ANTHU OYAMBIRA 10 KULEMBESA AZAKHALA NDI MWAYI OPASIDWA MA AIRPODS NDI NOTEBOOK AND PEN.

MUKAFUNA KUZIWA ZAMBIRI M***A KUYANKHULA NDI AGAMA CREATIVE PA 088 492 5896 OR CEASER PA +27813856112

Address

Blantyre
000000

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Chipa Tech posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Chipa Tech:

Shortcuts

Share