24/06/2025
Wawa 📩
Nakhala kwa zaka osakuyakhulani anthu aku NAMADIDI komaso onse Ali pa Page ino.
Ena kumati ndinasiya zokhoza ma fon, YAKHO sinasiye ndili kukono pa nsika wa namadid malo Pa Devie Kamanga.
Bwelani ndi ma fon anu kwa ine simuzakhumudwa ndi zakhoza mene mukufunira.
𝐙𝐢𝐤𝐨𝐦𝐨 𝐧𝐨𝐧𝐬𝐞