2days Electronics & GSM Tech

2days Electronics & GSM Tech {We are explorers of fast-moving world of electronics}

05/02/2026
old days
05/02/2026

old days

Mnyamata wa zaka 16 wapulumuka ku ngozi. Akuti nzake amaseweletsa spear gun. Ndiye mwangozi, muviwo unafwamphuka ndi kuk...
02/11/2025

Mnyamata wa zaka 16 wapulumuka ku ngozi.

Akuti nzake amaseweletsa spear gun. Ndiye mwangozi, muviwo unafwamphuka ndi kukalasa mmutu mwa nzakeyo. Unachita kulowela mbali ina ndi kukatulukila mbali ina ya mutuwo.

Madokotala anakwanitsa kuwuchotsa muviwo, omwe unali 8 inches. Kenako anamujambulanso kuti awone ngati ubongo wake uli bwinobwino.

Zotsatira zinaonetsa kuti mwanayo akhala bwinobwino chifukwa muviwo unalasa mbali yaku manja yomwe simapanga control zinthu zofunikira kwambiri.

25/10/2025

Old woman are sweetheart than young ones.

Address

Box 135, Bvumbwe
Thyolo
M1ROAD

Opening Hours

Monday 08:00 - 17:00
Tuesday 08:00 - 17:00
Wednesday 08:00 - 17:00
Thursday 08:00 - 17:00
Friday 08:00 - 17:00
Sunday 08:00 - 17:00

Telephone

+265999087387

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when 2days Electronics & GSM Tech posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to 2days Electronics & GSM Tech:

Share