01/01/2026
Salām 'alaykum wa Rahmatullāh wa Barakātuh
Tiziwe kuti ●:As-Salām Mu'allim Training Institute tsopano yasintha dzina ikutchedwa kuti ● As-Salām Institute Of Education
Mmalo mwa bungwe la , lomwe limagwira ntchito yoitanira anthu ku Chisilamu
(Da’wah) mwa chikondi, umunthu, ndi nzeru zomveka.
Ngati , timakhulupilira kuti Msilamu aliyense amene ali ndi udzindikiri wa
Chisilamu akhonza kuchita ntchito ya Da’wah ngati ali ndi mtima wodzipereka.
Pofuna kukulitsa ntchito komanso mapulogalamu athu ndi cholinga chofikira anthu
ambiri m'madera osiyanasiyana, yakonza ma interview kuti tipeze anthu omwe
angafune kugwira ntchitoyi.
Zokhudza Interview imeneyi
● : As-Salām Institute of education
● : 3 January 2026
:
● : Kuyambira 9:00 m'mawa
Zofunikira kwa omwe akufuna kudzapanga nawo interview
● Certificate ya maphunziro a
● Certificate ya maphunziro a Chisilamu ( ) kapena
● yopangidwa print
● Chiphatso cha
Modzichepetsa, tikupempha inu ngati adindo kuti mutithandizire kuti uthengawu
uwafikire anthu a mziki
Aziz Akhter
Head of Operations
iERA
1islamTv polumikizana nafe pa
+265 884 294 188