19/03/2015
Tili ndi kope printer imene omapanga copy ma documents ambiri pa nthawi yochepa. Nkhani yabwino kwa masulu ozumgulira Liwonde Mayeso anu atha kupangidwa panthawi yochepa pamtengonso wozizila. Ream lanu K2500 kukopela ream lonse. Ngati mulibe mapepala ndi K5 pa page kwa anthu okhala ndi ma documents ochuluka otha ma ream 10 above