Wa Ganyu. Mw

Wa Ganyu. Mw Working towards greatness

08/01/2026

we are available for all electrical faults

08/01/2026

we are available for all elections faults

08/01/2026
19/12/2025

anzanu nde akutiyana nanga inu mukutsala pati

Ife ndi akadaulo pokonza magetsi ndi madzingati mukufuna kuziwa zambiri timimbileni phone 0995828737
15/12/2025

Ife ndi akadaulo pokonza magetsi ndi madzi
ngati mukufuna kuziwa zambiri timimbileni phone 0995828737

NEBA ULIBWANJi ?lero kwandichela molemba kalati iyi chonde iwelenge modekha usapange phumachoyamba ndati ndikuziwitse ku...
11/12/2025

NEBA ULIBWANJi ?
lero kwandichela molemba kalati iyi chonde iwelenge modekha usapange phuma

choyamba ndati ndikuziwitse kuti ine kuno ndi nana komaso alamwako tilibwino
komaso nyumbayathu ilibwino kupa ifeyo

chachiwiri ndati ndikukumbutse kuti holide ija ikuyamba sabata likubwelali ndepajatu kumadzadza alendo kunyumba kwako nde uthenga wanga kwaiwe neba uli motele itana waganyu azakonze sink yako ina blocker ija toilet ija isaonekeso mwa unve komaso ma payipi amadzi ana booka aja aikidwe ena.
pakhomo pazisililika neba alendo aziiwala kwawo akabwela

ITANANI WAGANYU LERO (WAGANYU MW)
odalilika
osunga nthawu
okunva mavuto anu

plumber mbambande ndi ifeyo

tcayani lamya 0995828737

Are you looking for a professional plumber?Wanganyu Malawi is the answer to all your plumbing needs. We are the best in ...
09/12/2025

Are you looking for a professional plumber?
Wanganyu Malawi is the answer to all your plumbing needs. We are the best in the industry, offering quick and guaranteed plumbing services you can rely on.

Tipatseni za wiringzo ifeyo tigwire zimenezo for more whatsapp or call 0995 82 87 37.
28/11/2025

Tipatseni za wiringzo ifeyo tigwire zimenezo for more whatsapp or call 0995 82 87 37.

Address

Area 23
Lilongwe
806

Telephone

+265995828737

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Wa Ganyu. Mw posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Wa Ganyu. Mw:

Share