Laptop Msika Malawi

Laptop Msika Malawi Your trusted laptop market

📍Upstairs , shop no 48, Olympic mall, Behind game complex, Lilongwe

She came straight to our shop with one mission — to surprise her mum with a new laptop. Some gifts mean more than words....
23/09/2026

She came straight to our shop with one mission — to surprise her mum with a new laptop. Some gifts mean more than words.
Thank you for trusting us to be part of the surprise!

Team “Surprise”

Find us at Olympic Mall behind Game complex in room 48.

0993 391 708
0991 991 496



Akasi, We are OPEN !! We have ; LAPTOPS, LAPTOP CHARGERS, LAPTOP BAGS, KEYBOARDS, HEADPHONES and many accessories. Find ...
23/09/2026

Akasi, We are OPEN !!

We have ; LAPTOPS, LAPTOP CHARGERS, LAPTOP BAGS, KEYBOARDS, HEADPHONES and many accessories.

Find us at Olympic Mall behind Game complex in room 48.

0993 391 708
0991 991 496

Happy new Week, Happy customer. Apatseni ma congratulations akasiAkuti samafuna kuti mwana wawo azikavutika kuschool nde...
21/09/2026

Happy new Week, Happy customer.
Apatseni ma congratulations akasi

Akuti samafuna kuti mwana wawo azikavutika kuschool nde amugulira laptop yolimba battery, ya touchscreen, yasize yabwino, yaspeed komanso yolimba kuti mwana mpaka azamalize school asanakambilanenso za laptop..

Tipezeni pa olympic mall, kuseli kwa Game complex mu room number 48.

0993391708/ 0991991496



# lenovo

Big congratulations to our happy customer on the new laptopThank you for choosing us and trusting our Shop. We’re open e...
19/09/2026

Big congratulations to our happy customer on the new laptop
Thank you for choosing us and trusting our Shop.
We’re open every Saturday until 2 PM
come through and get yours.

Inu mufuna laptop yanji?
Tipezeni pa Olympic Mall kuseli kwa Game upstairs Room number 48.

0993 391 708
0991 991 496

LAPTOP YA LERO! - DAY 6Akasi, tikupitila kukubweletselani zabwino zosiyanasiyana. Lelo kuli machine amenewa Dell Latitud...
19/09/2026

LAPTOP YA LERO! - DAY 6

Akasi, tikupitila kukubweletselani zabwino zosiyanasiyana. Lelo kuli machine amenewa Dell Latitude 5490.

Intel Core i5 – 8th Gen, 8GB RAM, 256GB SSD

Akasi! Zabwino inu ayi?

Tipezeni Ku The Laptop Market, Olympic Mall Shop #48, upstairs, kuseli kwa Game Complex.

0993 391 708
0991 991 496

Laptop of the Day #6

Khaa 📸 Apatu munthu wamkulu ali happy ndi Machine omwe wagula.. Inu mufuna laptop yanji? Tipezeni pa Olympic Mall kuseli...
18/09/2026

Khaa 📸
Apatu munthu wamkulu ali happy ndi Machine omwe wagula..

Inu mufuna laptop yanji?
Tipezeni pa Olympic Mall kuseli kwa Game upstairs Room number 48.

0993 391 708
0991 991 496

LAPTOP YA LERO! - DAY 4 Akasi, mwina mumaona ngati Kuli ma Lenovo okha. Ayitu, ife ndi self contained Msika wa ma Laptop...
18/09/2026

LAPTOP YA LERO! - DAY 4

Akasi, mwina mumaona ngati Kuli ma Lenovo okha. Ayitu, ife ndi self contained Msika wa ma Laptop. Ndipo lelo takubweletserani HP Probook 640 G3.

Intel Core i5 – 7th Gen, 8GB RAM, 256GB SSD

Tipezeni ndithu Ku The Laptop Market, Olympic Mall Shop #48, upstairs, kuseli kwa Game Complex.

0993 391 708
0991 991 496

Laptop of the Day #4

LAPTOP YA LERO! - DAY 3 Lero tikusintha zinthu pang’ono! Takubweretserani Lenovo ThinkPad Yoga 460, laptop ya 2-in-1 yom...
17/09/2026

LAPTOP YA LERO! - DAY 3

Lero tikusintha zinthu pang’ono!

Takubweretserani Lenovo ThinkPad Yoga 460, laptop ya 2-in-1 yomwe mungagwiritse ntchito m’njira zosiyanasiyana.

Intel Core i5 – 6th Gen, 8GB RAM, 256GB SSD

Laptop ya touch, yobwela ndi Ka stylus pen komanso yopindika mbali zonse. Akasi ma set a clean a smart awa.

Laptop imodzi, njira zambiri zogwiritsira ntchito!

Tipezeni Ku The Laptop Market, Olympic Mall Shop #48, upstairs, kuseli kwa Game Complex.

0993 391 708
0991 991 496

Laptop of the Day #3

Akasi tangoganizani Mouse a Bluetooth, ogwira olo mutakhala 10 meters away from your laptop, 1000/1200 DPI high precisio...
16/09/2026

Akasi tangoganizani Mouse a Bluetooth, ogwira olo mutakhala 10 meters away from your laptop, 1000/1200 DPI high precision and resolution, ma battery anamakhala mpaka 4 months asanathe.

Mouse amenewo ndamene mukufunika ndipo ife tili nawo pa Olympic mall kuseli kwa Game mu Room number 48.

0993 391 708
0991 991 496


Join our sales team !
19/05/2026

Join our sales team !

Address

Lilongwe
207201

Opening Hours

Monday 08:30 - 17:30
Tuesday 08:30 - 17:30
Wednesday 08:30 - 17:30
Thursday 08:30 - 17:30
Friday 08:30 - 17:30
Saturday 08:30 - 17:30

Telephone

+265994052813

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Laptop Msika Malawi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Laptop Msika Malawi:

Shortcuts

Share