21/08/2026
'Unali Kuti' and 'Ndayesetsa' Hitmaker, Battafly yemwe anasowa pakatipa osatulutsa nyimbo iliyonse, sopano wabweraso mwatsopano ndi dzina lomwe wasitha pano ndi Ovyas.
Iye wati pompano akhala akugwetseso nyimbo zabwino monga kale lija. Anasowa uyu, tiyeni timulandireni. Welcome back Oviyasi 👏🏾