STIX Multimedia Centre

STIX Multimedia Centre Printing Services

Internet Services
Printing services
Photocopying services
Binding
Lamination
Scanning
Computer Hardware & Software repairs
Logo & Business Cards design & print

25/11/2025
27/08/2025

Celebrating my 13th year on Facebook. Thank you for your continuing support. I could never have made it without you. 🙏🤗🎉

MWAYI WAMAPHUNZIRO A COMPUTER KUYAMBIRA MWEZI WA JUNEONSE OLIPIRA PANO TISANAFIKE JUNE AZALIPIRA K50,000TIPEZENI KU CHIC...
07/05/2025

MWAYI WAMAPHUNZIRO A COMPUTER KUYAMBIRA MWEZI WA JUNE
ONSE OLIPIRA PANO TISANAFIKE JUNE AZALIPIRA K50,000
TIPEZENI KU CHICHIRI TRADE FAIR STAND NO. 74B
CALL/ APP 0888988071.

Training ija nde ikuyamba mawali, Tuesday 04 March, 2025.Bwerani tizayambire limodzi. Bwerani ndi laptop yanu, ngati pal...
03/03/2025

Training ija nde ikuyamba mawali, Tuesday 04 March, 2025.
Bwerani tizayambire limodzi. Bwerani ndi laptop yanu, ngati palibe muzagwiritsa ntchito aschool..osayiwala polembera.
See you at 8:00am sharp

Kodi mukufuna mutaphunzira Computer?? Ife a STIX MULTIMEDIA CENTRE takubweretserani mwayi ophunzira Computer kwa Mwezi p...
18/02/2025

Kodi mukufuna mutaphunzira Computer?? Ife a STIX MULTIMEDIA CENTRE takubweretserani mwayi ophunzira Computer kwa Mwezi pa Mtengo wa K75,000. Timalora kupereka kawiri pamene mukuzayamba ndikumalizitsa mkatikati mwamaphunziro anu.
Timalembetsa mayeso omwe mukakhonza mumalandira Certificate.

Tikupezeka mu Trade Fair Grounds, Chichiri.Mu mzinda wa Blantyre.

Kuti mudziwe zambiri imbani phone kapena tumizani message pa whatsapp pa number iyi: 0888988071

MAPHUNZIROWA AZAYAMBA PA 4 MARCH 2025!!!

Iyiyi bwerani muzayambire limodzi ndi anzanu.February Class
05/02/2025

Iyiyi bwerani muzayambire limodzi ndi anzanu.
February Class

27/12/2024

2025 Classes will start on 6th January

Wina ameneyo boss,muyimilireni ku Machinjiri Area 7- Chikapa
21/11/2024

Wina ameneyo boss,muyimilireni ku Machinjiri Area 7- Chikapa

Be addicted to your passions
Not your distractions

Registration for the November class is underway, classes will commence on 4th November
30/10/2024

Registration for the November class is underway, classes will commence on 4th November

Address

TRADE FAIR GROUNDS STAND NO. 74
Chichiri

Opening Hours

Monday 07:00 - 17:00
Tuesday 07:00 - 17:00
Wednesday 07:00 - 17:00
Thursday 07:00 - 17:00
Friday 07:00 - 17:00
Saturday 08:00 - 13:30

Telephone

+265888988071

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when STIX Multimedia Centre posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to STIX Multimedia Centre:

Share

Category