26/04/2026
FDH yasiya kuthandiza Sports ku Malawi
Bank ya FDH yalengeza kuti yasiya kutenga mbali la chilichonse chokhudza masewela(Sports) kutsatira kulepheleka kwa FDH Bank Premiership Launch dzulo pa bwalo la Kamuzu Stadium.
Izi zadza panthawi imene Pali matukutuku pakati pa bungwe la SULOM komanso FAM
Video๐?
https://malawi247.blog/watch.php?id=1595