Finaltouch

Finaltouch finaltouch IT & Electronics is Malawi's best repair shop for computers and other electronic gadgets.

Have you ever received an SMS from FINALTOUCH?If not… maybe you haven’t trusted us with your device yet And if you haven...
09/05/2026

Have you ever received an SMS from FINALTOUCH?

If not… maybe you haven’t trusted us with your device yet

And if you haven’t received any update lately, don’t worry — it simply means there’s currently no new progress on your repair.

At FINALTOUCH IT & Electronics, we keep you updated every step of the way with instant SMS notifications — from diagnosis, repair progress, testing, all the way to collection.

No chasing technicians
No unnecessary calls
No guessing what’s happening with your device

Just simple, professional, real-time repair updates straight to your phone



Muli bwaaaa? Remember Sabath and keep it holy.
09/05/2026

Muli bwaaaa?
Remember Sabath and keep it holy.


Nthawi zina kumupatsa mpata munthu kuti adyeko ndalama yanu posinthana ndi ma skills ake ndibwino. Akuti amatha kukhonza...
08/05/2026

Nthawi zina kumupatsa mpata munthu kuti adyeko ndalama yanu posinthana ndi ma skills ake ndibwino.

Akuti amatha kukhonza okha kkkkk.

Vuto lili part m'mene wapangira mazthuyu? Techs will understand with 5 seconds.



Don't worry ngati munasiya katundu kuti tikhonze ku finaltouch mulandira notification. Ena alandira kale ma text owauza ...
08/05/2026

Don't worry ngati munasiya katundu kuti tikhonze ku finaltouch mulandira notification.

Ena alandira kale ma text owauza kuti zatheka azatenge .


Tinakusowani pa page pano. Kwa a friday tiyeni. A Saturday and Sunday tikumanenso mawa ndi linalo
08/05/2026

Tinakusowani pa page pano. Kwa a friday tiyeni. A Saturday and Sunday tikumanenso mawa ndi linalo

UTAMBWALI UPOSE APA? Bwanji mukuchita kudzitsekera osamagwirira ntchito poyerapa kuti tonse tiziona zomwe mukuchita?Yes ...
04/05/2026

UTAMBWALI UPOSE APA?
Bwanji mukuchita kudzitsekera osamagwirira ntchito poyerapa kuti tonse tiziona zomwe mukuchita?

Yes its true kuti ma Technician ena amatengerapo mwayi opanga zofoila pa katundu wa ma customer coz customer sakuona zomwe zikuchitika kuseriko, koma palinso zifukwa zokwanira zomwe
ife ngati Finaltouch komanso ma repair shop ena amagwira nchito behind the wall.

1. Focus.
tangoganizani munthu akumasula laptop, customer amvakere bwinotu muzitsekula bwino muyamba kuiphwanya yet vuto lomwe labweralo lifunika kumasula kumene. Ntchito zina zimafunika kugwiridwa modekha komanso mwachidwi izi zimathandiza kuchepetsa ma errors/mistake during the repair process.

2. Controlled environment.
Eyetu Technician akugwira nchito kwinatu customer waika botolo la thobwa pa bench yomwe pakugwiridwa ntchito mpaka technician kuchita kupempha ku guys tasunthani wez pali m'dima i need some light. Pa workbench pakakhala kuti Technician ndi amene alipo yekha kumakhalanso kosavuta kupanga organize zinthu coz ma customer ena amamubalalitsa Technician akamagulugusha

3. Safety.
Amzanutu anapysa atagwira soldering iron yotentha. Ndiye zina kumakhala kuteteza ma customer ku zinthu zamoto monga ma hotair etc. Enanso amadandaula ndi ma fungo ochokera ku zinthu zomwe timagwiritsa ntchito monga flux ndi soldering wire etc.
Nthawi zina kumaphulika zinthu monga ma capacitor etc izitu muzidziwa.

4. Mbava.
Simacustomer onse omwe amakhala ndi intention ya bho ena amabwera kuzaiwerenga kuti azabe mosavuta. enanso amatha kubwera ndi kantchito konamanama just to distruct the technician kwinaku akuba zinthu za ma customer ena . Mukudziwa kale technician amakhala kuti watsekula zinthu zingapo. Enanso amatha kuba ma screwdriver ndi ma tools ena odhula.

5. Shiiiiiii izi ndi ndiye musaulule kkkkk
Ma customer ena amaphweketsa ntchito chifukwa choti siinatenge nthawi pokhonza. For exapmle kubwere customer akudandaula kuti laptop yake yangozima siikuyakanso, technician kungotsekula kupanga reset CMOS boom yatheka, zikatele ena amafuna kuchuluka mzeru, koma akakhala kuti technician amapangira kukachipinda komata amaona zokamuuza customer uja kuti onse asangalale.


Ifetu a Finaltouch tinayamba tayeserapo kugwira ntchito pa open koma zinatilaka koma tinaika ndondomeko kuti
ma customer athu azikhala okhutira ndi ma service athu ngakhale kuti nthawi zina timakumana ndi timavuto mwa apo ndi apo ndipo omwe anabwera atha kuchitira umboni kuti;

1. Tisanayambe kugwira ntchito customer amalemberedwa Repair ticket yomwe imakhala ndi ma details monga RAM,HDD charger ndi zina. Ticket imeneyi imagwiritsidwa tchito panthawi yomwe device ikutengedwa popanga verify zomwe zinabwera ndi zomwe zikutengedwa.

2. Customer amapatsidwa mwayi oti ayike zizindikiro pa katundu wake ndipo akamatenganso amapanga verify

3. Tchito zina zosafunika kumasula timapangira poyera. Windows kaya ma package timapangira poyera unless ngati pali zinthu zofunika attention kwambiri.

NOTE: Palibe repair shop yopanda mavuto kapena kuti ma claim.

Inuyo muli ku mbali iti Technician azigwirira nthito poyera or ayi??

Ka wire akaka kamakhala kakatalitu, m***a kupangira separate ma LCD a phone/laptop ambirimbiri. Phindu lomwe mungapeze n...
04/05/2026

Ka wire akaka kamakhala kakatalitu, m***a kupangira separate ma LCD a phone/laptop ambirimbiri. Phindu lomwe mungapeze ndiloposa ka 10 pin komwe mungaspende pogulira mishani imeneyi.

Ma technician inu muzidziwika ndi ntchito za clean. Pezani touch separating wire wanu ma details ndi omwe ali pa image yo.



You change your car’s oil before the engine knocks.You replace filters before they clog.You top up battery water before ...
02/05/2026

You change your car’s oil before the engine knocks.
You replace filters before they clog.
You top up battery water before it dies.

Why?

Because you understand one simple truth: maintenance is cheaper than repair.

Now think about your computer…

It’s working every day.
Handling your business, your files, your money.
But inside?

Dust is building up.
Fans are choking.
Thermal paste is drying out.
Heat is slowly damaging your motherboard, processor, and storage.

And just like a car…
You won’t notice the damage until one day:

It becomes slow, starts overheating, shuts down randomly or worse… it completely dies

At that point, you’re no longer talking about maintenance…
You’re talking about expensive repairs or total replacement.

A simple preventive service can improve speed and performance, extend your computer’s lifespan, prevent sudden breakdowns, protect your important data and save you money in the long run

Don’t wait for your computer to “break” before you act.

Take care of it like you take care of your car.

Book your Preventive Maintenance today
Call 0981 553 576 or Whatsapp 0884 55 35 76
www.ft-mw.com

FinalTouch — We don’t just fix problems, we prevent them.



When is the right time to mark a device as fixed?Nthawi zambiri ma Technician timaganiza kuti pamene customer watenga ka...
01/05/2026

When is the right time to mark a device as fixed?

Nthawi zambiri ma Technician timaganiza kuti pamene customer watenga katundu wake and walipira ndiye kuti business yathela pamenepo basi.

Mayaz simabusiness onse amene amatha mwa choncho, nthawi zina zimatheka customer kuyimba phone atangofika kwawo kumadandaula kuti vuto lomwe limakhonzedwa silinatheke ndiye uzachimva china chikuti "Aaaaa zimenezo ndi zako mesa kushop kuja tinakuyesera ndipo unaona chikugwira ntchito??? Zimenezo ndizachamba usandibhowe",
Zinthu izi zimaipitsa mbiri ya ma Technician.

Ku Finaltouch, we believe kuti customer azikhala ndi nthawi yokwanira kuti apange confirm kuti vuto lomwe anabwera nalo latheka kufikira pomwe wakhutitsidwa. This is when we mark a business as successfull.

Technician akagwira ntchito yabwino komanso akamupanga treat customer mwa dongosolo ngati bwana wake, Customer amakhala osangalala ndipo amafalitsa zabwino.

Guaranteeeeeeeee! Guaranteeeeeeeee! eyetu guarantee ndi njira yomwe Technician amayenera kupereka kwa customer after kugwira ganyu, its not by force or compulsory kuti
paziperekedwa guarantee, mayaz koma ngati Technician akuziguguda pantima kuti wa runner dancell ya bho why not giving a guarantee. Komansotu guarantee siimakhala ya forever.

NOTE : Sizonse zomwe zimayenera kukhala ndi guarantee. Eti munthu amaikitsa Windows ndiye guarantee azifuna yachani inu aaaa.

Guarantee siimakhalapo ngati customer amayesera kukhonza yekha vuto after Technician atagwira kale ntchito yake. Customer akagwetsa kapena kunyowetsa device after repair sitimalora ife.

Komansotu ma customer ena amadabwitsa umva akuti tandiikira Windows mu laptop yangayi kenako abwere after weeks mkumati laptop yangayi mutangoigwira muja inasiya kutchaja kkkkk komabe tonse ndi anthu timakhala ndi zofooka tiyeni tizikambirana mwa bho bho osati kumangokangangana.

Inu mukuona bwa????????


Jumuah Mubarak to all Muslims.
01/05/2026

Jumuah Mubarak to all Muslims.



Timakunyadirani nonse........
01/05/2026

Timakunyadirani nonse........



Address

Livingstone Avenue Limbe
Blantyre
312229

Opening Hours

Monday 08:30 - 17:00
Tuesday 08:30 - 17:00
Wednesday 08:30 - 17:00
Thursday 08:30 - 17:00
Friday 08:00 - 17:00
Saturday 09:00 - 14:00

Telephone

+265884553576

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Finaltouch posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Finaltouch:

Share

Category