PKM Design

PKM Design Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from PKM Design, Graphic designer, Blantyre.

25/02/2026

With Agora Limited – I'm on a streak! I've been a top fan for 5 months in a row. 🎉

19/01/2026
25/09/2025

Tsoka kwa omwe amadikilira ma 500,000 sibasi akusiyani pa dzuwa kapena ndisafulumire kunena Pali njira Ina?

22/09/2025

Aliyense njila yake ndiyosiyana ndi wina

Mayi awa ndi Graça Machel. Mayi yekhayo yemwe anakhala first lady wa mayiko awiri osiyana.

Anali mkazi wa Samora Machel ku Mozambique (1975–1986).

Kenako anakwatiwa ndi Nelson Mandela ku South Africa (1998–2013).

Ndi mayi olimbikira payekha.

Anavekedwa title ya Dame Commander of the Order of the British Empire mu 1977, ndi Queen Elizabeth ll chifukwa cha ntchito yake ya women and children's rights.

Sidenote
You are whatever you believe yourself to be

22/09/2025

Anyamata mukuwaonawa awamanga week ino kaamba komachita chipongwe(kulanda ndikuba pogwiritsa ntchito mpeni) anthu ntaunishipi ya Limbe.Anyamatawa ndi a zaka za pakati pa 13 ndi 18 ndipo amangidwa kumathero a sabata yangothayi atatsinidwa khutu.

29/09/2024

Company ya Bata ku Kenya yakwanitsa kupanga ma pair awili a nsapato zazikulu kwambili zomwe sanapangeko chiyambile, nsapatozi ndi za size 21 ndipo zapelekedwa mwa ulele kwa nyamata otchedwa Bradley Mallongo. Nyamatayu akuti ndi wamtali kuposa aliyese mu dzikolo ndipo wakhala akudandaula kuti amayenda movutika chifukwa samapeza nsapato za saizi yake kamba koti phanzi lake ndialikulu kwambili.

10/12/2023
25/08/2023

BREAKING NEWS


MWANA WA MASIKINI WAPHEDWA

M'mawa wa lero ana amasikini atatu anavulaza ndikulanda bambo wina katundu wake pomwe amadutsa nsewu mudi via makhetha.

Bambowa alandidwa ndalama, nsapato komanso avulazidwa pobayidwa ndi mpeni nkhope.

Polimbana ndi anawa, iwo adakwanitsa kugwila mwana mmodzi ndipo anakuwa kupempha thandizo mpomwe khamu la anthu lidatulukila.

Anthu achifundo adakwanitsa kuwatengela bambowa ku chipatala ndipo ena anayamba kumenya mwanayo mpaka kupha.

Address

Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when PKM Design posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share