Transcribed tales

Transcribed tales FOREX TRADER AND FONTEND WEB DEVELOPER

25/03/2026

Version 2.0 of THE NIGHT COMES FOR US. New movie coming soon

24/03/2026

HELLO GUYS, WE'RE BACK 🔥

TICHOSENI UMBULI. KODI UYU MUKUTI ZAKHALA BWANJI
10/12/2025

TICHOSENI UMBULI. KODI UYU MUKUTI ZAKHALA BWANJI

Akulu akulu, history is the best teacher
08/12/2025

Akulu akulu, history is the best teacher

05/12/2025
Nkhani yonse ilimotere.Mwanayo dzina lake ndi Syuphanda Xhoja, pamene amayi a akulowo ndi a Meeiyex Thindwazo. onse ndi ...
04/12/2025

Nkhani yonse ilimotere.

Mwanayo dzina lake ndi Syuphanda Xhoja, pamene amayi a akulowo ndi a Meeiyex Thindwazo. onse ndi aku South Africa.

Linali Friday sabata yatha pamene anajambula kanema wawo ulawula omwe ukuzungulirawo. Kuti zifike apa ati Amayi a akuluwo ndi a Part time teacher pa Sukulu yomwe mwanayo amaphunzira. Ndipo pa tsikulo anamuuza mwanayo kuti lero ukawanamize makolo ako ngati ukupita ku Sukulu nzabwera pa Galimoto kuzakutenga ukazifika pa "Dinner Swim Dinning.' ku South Africa.

Izi zinachitikadi koma mwanayo ngati wam'muna samaziwa zoti amayi wo omwe anali mphuzitsi wake akufuna kuti atani naye koma iye anawakhulupilire amapanga chilichonse amuuza.

Atafika kunyumba kwawo ubwino wake ndi single lady. mphuzitsi yo anamuuza zoti akufuna S*x koma akufuna achite yojambula video yomwe mzungu wina waku Australia anawauza kuti akajambula video yolaula ndi mwana azawapasa $500,000 Dollars. ndipo akajambula onse azagawana Iwo anamukhulupilira chonchi chifukwa mbuyo monse amati akamutumizira video akusamba amawatumizira ndalama.

The boom.!!!makolo a mwana akayisuma ku court kuja koma mwana wati awasiye iye wawakonda ndipo mwana wachita kuwauza a Police kuti Mayanga asakunamizeni kuti sindinafike dzaka 18. Iye wauza a Police kuti alindi dzaka 21. Pomwe mayake akuti mwanayo ndiwa dzaka 17. ndi mulandu amugwilira mayiwo amangidwe. Koma poti Mayiwo ikuwoneka ngati ndi against nawo angozisiya poti yekha mwanayo akuyiyankhuliraso udyo kwa Police.

Ma lesson onse omwe tapanga kale omwe tingawonere pofuna kuphunzira kupanga website. Visit www.mwtether.online . Osaopa ...
30/11/2025

Ma lesson onse omwe tapanga kale omwe tingawonere pofuna kuphunzira kupanga website. Visit www.mwtether.online . Osaopa ma videos onse ndi less than 35mb, ambiri ndima 10 mb to 16 mb.

Ma lesson onse tiwaponya ku website (https://mwtether.online) muzikawapezera komweko. Izi zithandiza kuti muzikwanitsa k...
28/11/2025

Ma lesson onse tiwaponya ku website (https://mwtether.online) muzikawapezera komweko. Izi zithandiza kuti muzikwanitsa kuwapanga download nkumawonera nthawi yomwe mwazimitsa data komanso kuwasunga mu phone mwanu. Pakadali pano muziwapezera pa categories ya entertainment ( temporarily).

Check the sample
follow Transcribed tales
Technologia

Sitili safe
26/11/2025

Sitili safe

💛💛💛
26/11/2025

💛💛💛

Address

Zomba
Blantyre

Website

http://www.mwtether.online/

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Transcribed tales posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category