Mechro

Mechro Mechro Limited - Innovating Agriculture! Embark on a journey where tradition meets innovation, and technology harmonizes with the land.

As an agile & forward-thinking agriculture technology company, our mission is to redefine the very essence of farming.

You worked the season. Don’t let the store steal it.Nkhokwe hermetic bags help lock in what you harvested.Next batch com...
31/07/2026

You worked the season. Don’t let the store steal it.

Nkhokwe hermetic bags help lock in what you harvested.
Next batch coming! WhatsApp +265 881 606 174 to join the interest list.

Ask for Nkhokwe. Share this with one farmer who needs it.

Lero tayika Munda AI Hub ku demo farm yathu ku Blantyre. 🌱Chipangizochi chimathandiza kudziwa zomwe nthaka ikufuna kuti ...
24/06/2026

Lero tayika Munda AI Hub ku demo farm yathu ku Blantyre. 🌱

Chipangizochi chimathandiza kudziwa zomwe nthaka ikufuna kuti mlimi athe kupanga zisankho zabwino asanagwiritse ntchito ndalama pa feteleza kapena zinthu zina za ulimi.

Mbatata zomwe mukuona mu Nkhokwe Bag zinakulira pa nthaka yomweyi. Kuyambira lero, masensa ayamba kusonkhanitsa deta yomwe itithandize kumvetsa bwino momwe nthaka ikuyendera komanso momwe tingathandizire alimi kukolola bwino.

Ulendo wa zokolola zabwino suyambira pokolola, umayambira pa nthaka.

Ndipo ulendowu wayamba lero. 🇲🇼

Nkhokwe, thumba la a Malawi. 🌽Kodi mukudziwa kuti mpaka 30% ya chimanga, nyemba, nandolo, kapena khobwe wanu chimaononge...
28/05/2026

Nkhokwe, thumba la a Malawi. 🌽

Kodi mukudziwa kuti mpaka 30% ya chimanga, nyemba, nandolo, kapena khobwe wanu chimaonongeka chaka chilichonse? Osati kumunda, koma ku nkhokwe kapena mmatumba anu ngakhale muthire mankhwala ophera tizilombo tanankafumbwe?

Mechro Limited yapanga Nkhokwe Harvest Storage Bags kuti tithandize alimi kuno ku Malawi kusunga zokolola zawo bwino.

✅ Thumba la Nkhokwe la makilogiramu 50
✅ Limaletsa mpweya kulowa mthumba lanu. Kupha tizilombo tonse popanda mankhwala
✅ Sililola chinyontho kuti chilowe mthumba lanu. Chimanga chimatetezeka.
✅ Malangizo pa thumbali analembedwa mu Chichewa. Chifukwa timasamalira alimi a m'dziko la Malawi ndi maiko otiyandikira kuti agwiritse ntchito bwino.

Zokolola zimakhala zotetezedwa, kuthetsa kuonongeka kwa chakudya kuchoka pa 30% kupita pa 5% yokha!

Alimi oposa 6,500 ku Malawi akugwiritsa ntchito Nkhokwe Bags kale.

Mukufuna kusunga zokolola zanu bwino chaka chino? Tilankhuleni:

📞 +265 881 606 174
📧 [email protected]
🌐 mechro.io
📍Chichiri Trade Fair Grounds, Stand Number 5G, Blantyre

Matumbawa akupezekanso kwa ma agro-dealer otchuka mu mdela lanu.

When a freezer fails, you don't get a second chance 🧊🚨This morning at 10:15 AM, TempCras by Mechro detected a critical f...
27/05/2026

When a freezer fails, you don't get a second chance 🧊🚨

This morning at 10:15 AM, TempCras by Mechro detected a critical failure in an outdoor laboratory container.

The data:

Safe range: -30°C to -15°C
Detected temp: 5.5°C
Deviation: +20.5°C above maximum
The response:
TempCras instantly triggered a critical alert with exact remediation steps: check power, door seal, and compressor. Transfer contents if not restored within 15 minutes.

No waiting for the next manual log. No discovering the loss hours later.

This is TempCras by Mechro, real-time IoT monitoring that protects vaccines, lab samples, and cold-chain assets 24/7. Because in cold storage, minutes matter.

Want to prevent your own “5.5°C moment”?
👉 DM us or visit https://mechro.io/request-demo for a demo

Manual temperature checks are no longer enough.TempCras delivers:✅ Real-time monitoring✅ SMS and email alerts✅ Temperatu...
08/05/2026

Manual temperature checks are no longer enough.

TempCras delivers:
✅ Real-time monitoring
✅ SMS and email alerts
✅ Temperature logs and reports
✅ Secure remote access

See the future of cold-chain intelligence: https://tempcras.io

TempCras is a new innovative technology that makes it easy to track and monitor temperature of cold rooms, refrigeration systems and cold vans. It is a very easy system to install as well as to implement.

Address

Malawi Confederation Of Chambers Of Commerce And Industry (MCCCI), Chichiri Tradefair, Stand Number 5G
Blantyre

Opening Hours

Monday 08:00 - 16:30
Tuesday 08:00 - 16:30
Wednesday 08:00 - 16:30
Thursday 08:00 - 16:30
Friday 08:00 - 16:30
Saturday 08:00 - 11:30

Telephone

+265882399940

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mechro posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Business

Send a message to Mechro:

Shortcuts

Share