21/05/2026
Part 3
Zidatha bwanji bambo atapezelera nkazi wake ali pa mwamba pa mamuna wina nyumba yokhala yake kuchipinda chake bed ndi mattress ogula yekha kapenaso nyumbayo yolipira yekha???? 🫠🫠
kodi mamunayi akuganiza chani ???? 🤔😭😭
nayi nkhani yonse
Bambo adagona kuchipinda mayi sanawasatile amangolira pa sit room mpaka kugona pomwepo k*tacha mmawa bambo sadayankhule kathu ulendo wakuntchito kusiya ndalama yachakudya pa teburo munthu wamayi akugona mazulo pochoka kuntchito adangogona osalankhula kathu
Pak*ti ntchimo limazuza olichita munthu wamayi yekha yekha akamuwona mamuna wake amangoyamba kugwesa msozi uku ak*ti mundi khululukile bambo ndipo iye samayankha kanthu
Zonsezi zimachitika osamuuza aliyese wakwawo kwa nkazi even azibale ake amamunayo or azinzake poganizila k*t angamusokoneze maganizo muziwa aliyense akupase maganizo ake munthu umabalalika wina ak*ti uthese wina ukanamumenya wina usamukhulukukile etc 😏
Siku lachitatu bambo adanyamuka monga nthawi zonse kusiya yandiwo osalankhula mkumapita kuntchito. apa ndipomwe mayiwa anazimva k*ti ineyo kwanga kwatha😭😭😭
Adalemba kalata yosazika achibale komaso mamuna wake ndukufotokoza zonse zachitika osa nenapo boza. kenaka ndikumupepesanso mamuna wake chifukwa chomuswera mtima k*ti ngati kuli kotheka tizawonana😭😭😭
Mamuna pochoka kunchito adapeza maliro kuchipinda konkuja atazimanga kudenga pogwilisa ntchito bigili ngati chokwelapo ulendo ndi womweo.
Apolice ndi achibale adavomeleza k*t olakwa ndi.......✍️✍️ thank you so much guys
Follow my page for more beautiful stories