16/07/2024
" C. KENAKO E "
Matchaja ambiri ndiponso ma battery ena amalembedwa kachizindikiro aka ka C.E.
Mawuwa ndi chi French ndipo amalembedwa kuti " CONFORMITÉ EUROPÉENE" but mu English ndi EUROPEAN CONFORMITY. In short ndi chidindo Cha bungwe limene limapereka ma certificate ku makampane amene akupanga ma battery , mafoni ndi zida zina za makono zimene zimagulitsidwa ku MAYIKO onse amene Ali mu EUROPEAN UNION.
So kampani ikakwanitsa ziyenerezo zawo
Basi imapatsidwa mphamvu kugulitsa katundu wawo mmashop. Mukagula chinthu choti chili ndi chidindo icho mu shop komano ndi Cha fake, kapena chaotcha foni yanu m***a kudyapo K 2, 000, 000 apa. Lamulo limati mukamagula phone ya battery LOMWE Lili ndi chidindo ichi muzipatsidwa warranty ya 12 months ( 1 year ). So muli ndi ufulu omangitsa shop imene yakugulitsani foni ya fake yomwe Ili ndi chizindikiro ichi.... (Consumer Rights Directive (2011/83/EU).
Komano malamulo azasatidwa. Mukuziwa mafoni ati AMENE Ali ndi chidindo ichi ?
LIKE phone Repair & Accessories