28/03/2026
Tikukudziwitsani kuti 4G Router ya K30000 ikhala ikusowa pa msika yathu Airtel ku Malawi kuno. Panopa kuli 5G Router imane izikhala ya Airtel Company osati ya munthu aliyense kapena customer ayi, kuti munthu azigwiritsa ntchito 5G Connection; pazikhala kusayinilana mgwirizano pa form yathu.
Customer azipeleka connection fee ya K50000 komanso azigula Unlimited data bundle ya K100000 kapena K75000 a pa mwezi, onsewa ndi ma Data ofanana koma akusiyana kathamangidwe kake (speed).
Mukafuna kudziwa zambiri ndifunseni pa Whatsapp: 994353941