Mr zex S P tech

Mr zex S P tech Electronic and phone repair

16/02/2025

NGATI NDIMAVUTO NGATI AWA PAPHONE YANU BWERANI TIKUTHANDIZENI

network unlock

Password unlock

Google account bypass

IPhone icloud bypass

NDIZINA ZAMBIRI KANTENGO PANG'ONO

30/01/2025

Kugula lcd kapena internal battery ndizinthu zina kuika ulele

Ndili mumponela

30/01/2025

Buy your favorite accessories to mr zex s p tech

30/01/2025

Tikugulitsa ma phone accessories amaphone osiyanasiyana

Komanso kukoza maphone pa mtengo ovelera

Tili ndi

Charge

Battery

Lcd

Camera glass

Back cover

Switch

And etc

Pezani anu lero

Ma fast charger awa for all phones Kantengo pang'ono
19/01/2025

Ma fast charger awa for all phones

Kantengo pang'ono

Agulileni posha yabwino a girl friend anu phone iwale Kantengo pang'ono
19/01/2025

Agulileni posha yabwino a girl friend anu phone iwale

Kantengo pang'ono

Bluetooth speakers quality Kantengo pang'ono
19/01/2025

Bluetooth speakers quality

Kantengo pang'ono

19/01/2025

Mulibwanji ngati mukufuna ma phones accessories ama phone ossiyanasiyana ndipezeni simuzakhumudwa eg

Ma battery external and internal

Ma posha

Ma charge

Ma touchscreen

Ma LCD ossiyanasiyana

Ma Bluetooth speaker

Ma ponds

Ma headphones

Ma camera glass

Ma back cover

Ndizina zambiri inu mukundako chani?

Tilinso ndima suboofer komanso ma plasma ossiyanasiyana ngati

Hisense

LG

Dixon

Omega

Dgmacks

Huwa

And etc

10/12/2024

Kwazathu amene phone yanu ili ndimavuto awa around dowa ndipezeni ndizakuthandizani pa mvuto lanu

Mvuto LA LCD

Ngati phone yanu yalowa madzi kapena kugwera m'madzi

Phone yanu sikuyaka

Charge system

Ikungoyaka ndikuzima yokha

Phone flashing

Password unlock

Network unlock

Ndizina zambiri ngati mukufuna kuva zambiri DM me

Komanso ndili ndima LCD osayasiyana a mitundu yosiyanasiyana pa mitengo yabwino

Ma battery

Ma charge

Ma USB cable

Ma posha

Ma screen protector

Ma glass

Ma camera glass

Ma back cover

Ngati mwagula phone spair pats timachotsela mtengo poikira

07/12/2024

Kwa anthu amene mwazungulira mponela bwerani kwa Isaac phone repair kuti muzathandizidwe pavuto la phone yanu

Ndikupezeka pa mponela pafupi ndi nsika wa kalinda

Address

Mponela

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Mr zex S P tech posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share