06/08/2025
π’ GULANI MA PHONE A TECNO NDI ITEL PANGONGOLE π±
Ngongoleyi ndi ya aliyense amene ali ndi kuthekera kobweza pang'onopang'ono.
π Kumbukirani: Mtengo wa ngongole umakhala wokwera kuposa wa cash.
β
ZOFUNIKA:
1.Chiphaso cha uzika (National ID)
2.Ndalama ya deposit
π¦ Mukangopereka deposit, mumatenga foni nthawi yomweyo ndipo mumayamba kugwiritsa ntchito.
π΅ Ndalama yotsalayo imayamba kulipidwa pakapita masiku 7, ndipo mungasankhe kulipira tsiku ndi tsiku, sabata iliyonse kapena mwezi uliwonse.
π° M***a kulipira nthawi iliyonse ndalama yochuluka kuti mumalize msanga.
π± MA PHONE ALIPO NDI MITENGO YA NGONGOLE:
π TECNO:
POP 9 (64GB):
K156,200 DEPOSIT |
Phone yi kumailipila pa tsiku ndi ma MK2,050
Pamwezi ma MK61,500
POP 10C(64GB):
DEPOSIT MK144,000
Phone yi kumailipila pa tsiku ndi ma MK2,050
Pamwezi MK61,500.
POP 10 (64GB)
DEPOSIT MK144,000
Phone yi kumailipila pa tsiku ndi MK2,050
Pamwezi ma MK61,500
POP 10 (128GB)
DEPOSIT MK185,000
Phone yi kumailipila pa tsiku ndi MK2,700
Pamwezi ndi ma MK79,000.
SPARK GO 1 (64GB):
Deposit MK137,600
Phone yi kumailipila pa tsiku ndi MK1,959
Pamwezi MK58,700.
SPARK 40 (128GB):
K185,200 DEPOSIT |
Phone yi kumailipila pa tsiku ndi MK2,700
Pamwezi MK79,000.
CAMON 40 (256GB):
K424,000 DEPOSIT
Phone yi kumailipila pa tsiku ndi MK5,900
Pamwezi MK177,000.
π ITEL:
P65 (128GB)
DEPOSIT MK192,000
Phone yi kumailipila pa tsiku ndi MK2,800
Pamwezi MK84,000.
A80 (128GB):
K153,000 DEPOSIT
Phone yi kumailipila pa tsiku ndi MK2,187,
Pamwezi MK65,610.
A90 (128GB):
K150,800 DEPOSIT
Phone yi kumailipila pa tsiku ndi MK2,200
Pamwezi MK66,000.
P65C (128GB):
K144,000 DEPOSIT
Phone yi kumailipila pa tsiku ndi MK2,050
Pamwezi MK61,500.
π Tili ku:
Area 3 Game Complex,
Ku Area 25 Nsungwi, Lilongwe
π Lumikizanani nane pa:
0993 187 142
0885 199 185
π Nthawi Yogwira Ntchito:
MonβFri: 07:30 β 17:00
Sat: 07:30 β 17:00
Sunday - 07:00
π¦
Zikomo kwambiri π β