21/09/2026
Zomwe apanga atsikana awa zadabwitsa gulu:-
Iwowa atangolemba mayeso a 4 ndikukhonza anabwela kaye ku kuti azaphunzile Maphunziro a Computer_ICT Computer use.
Tikunena pano awiliwa akupita ku ma college osiyana siyana ndipo mmodzi wayambapo ntchito mu stationary and printing shop ku machinjiri.
Zosililisa ana achichepele chonchi kuphunzila luso ndikuyambapo kudyelera. Maphunziro ena ngati awa akuyamba so pa 12th October 2026. Zisakuphonyeni,
Lembetsani nanu ku ma center Sanwecka ngati mwalemba maphunzilo a 4 kumene.
Sanwecka Blantyre: Chichiri tradefair stand 33,
Sanwecka Lilongwe: falls, behind msonkhamanja CCAP (ex pact Campus)
Sanwecka Mzuzu: behind uncle Joze import & Export.
Call/whatsapp Sanwecka call center 0999 48 49 49 or +265888484949
Email: [email protected]