26/06/2026
Banja lina lipempha wantchito mimba. 2
Zidatha bwanji wantchito atapeleka mimba kwa abwana ake✍️✍️😒😒😒😒
Apatu banjali lidasangalara chifukwa lapeza chosowa chawo pak*ti ngakhale adali ndi chilichonse pakhomo pawo koma chitozo chawo chidali mphatso ya mwana.
Adatenga ndalama yosala ndikupeleka kwa m'nyamata uja apatu
Wantchitoyi adasiya pomwepo ntchito ndikuyamba ka business kake.
Bambo komaso mayi adayamba kugwira ntchito yosamalira mimba muja muziwira pamafunika zokudya ndi zokumwa pakusamala mimba, komso kugula zinthu monga ma bamesen zovala kungotchulapo zochepa
Apa wantchito adawawuza mayiwa k*ti sakuyenera kugonana ndimamuna wawo kuopa mimbayi angayisokoneze mamunayi choncho akafuna kugwiridwa ntchito yodyesera mimbayi akuyenera kumu ziwisa Wantchitoyi.
Zimathekadi mayiwa amayendera ngati chipatala ku nyumba ya mnyamatayu akafuna thandidzo😔😔
Nthawi yobadwa mwana idafika apa ndipamene khoswe sakondwa akawona mphaka 😄😄
Mayi uja atadwara usiku adanyamuka ulendo wakuchipatala adafikila kuchila usiku womweo sadachedwe mwana wobadwa wamamuna🥰🥰🥰
Mokodwera ndi chimwemwe adayimbira foni wantchito uja yemwe adapeleka mimbayo
Apatu wantchito adanyadila k*t ndi wobeleka pak*ti naye anali asada belekepo 🤔🤔
Nkhani idavuta ponena k*t nyamatayu apeleke dzina yekha komaso mwanayo azitchulidwa mudzina lake zomwe osamala mimba sada gwilizane nazo koma wantchito uja anati ngati sizitero ndiye aliyense nkhaniyi ayiziwa😭😭😭
Mukadakhala inu mukadatani???
Tapangani Like comment komaso follow page ino k*ti zambili zisamaku phonyeni osaiwala share please 🙏
Iyi 👉👉ndi youtu.be Chanel yanga ndipangen support popanga subscribe please 🙏🙏🙏https://youtube.com/?si=VFMnAjmqWrOxNLTa