Kàngàwàkàkò Technology

Kàngàwàkàkò Technology Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Kàngàwàkàkò Technology, Computer Company, Jenda Theo.

27/07/2022

Tikulitsa ma laptop pamtengo ongotora tchayani lamya pa +265 990453869 kuti mlankhure ndi Sells Maneger

Send a message to learn more

14/01/2022

takulandilani none ku Kàñgàwàkàkò Technology tiuzana zochita kwa amene akufuna kuphunzira 💻 computer

27/12/2021

Tipilidze pomwe tinasiyira

;Ataona kuti patelera ananjonjora inde Inu kuthawa ngati nkhanga, anayesera kumthamangisa koma sanampeze, pano akukhalira kubindikira mnyumba ngati Namwali .
phunziro. "Tikalakwirana ndibwino kukambirana kusiyana ndikupanga chipongwe"

Pangani Share Komanso .like. page yathuyi Nkhani Zabwino Komanso zochitisa chidwi zilipo.
mazulo. abwino.
Kàñgàwàkàkò.Technology.

27/12/2021

Moni Nonse
@ ndikulandireni ndi nkhani za msanguluso madzulo ano .

Tiyambe motere;
Mkulu wina ayenda chothamanga ngati wakuba phone, nkhaniyi ikuti :Mnyamatayu tsiku lina atalezera adayambana ndi anthu pamaro ena omwera mowa nde wina anammenya mpaka thapsaaaa!! Nde dzulo laliwitsiri anapita ku nyumba ya munthu anammenya uja kuti akabwenze chipongwe adampangira chija mwasoka anthu ena anamva nsanga za phokosolo ndipo atawona kuti m'bale wao akumenyedwa Sanaimve, mpaka analowelera ndewu ija ndipamene anazindikira kuti patelera ndipo

10/11/2021

am welcomed allof you to my business side. Be free and stay well

14/10/2021

Am teaching people Laptop for only 2500 came all

09/10/2021

We are the Masters in Computer science for more information please contact us on +265995509528 or +27789346819 For WhatsApp

Address

Jenda Theo

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Kàngàwàkàkò Technology posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share