Arclight Branding & Prints

Arclight Branding & Prints Professional branding, portrait photography, and print solutions that make your story stand out

31/07/2026

Good morning Akasi!

Osaiwala kopangitsa Ma Canvas Potrait A QUALITY kuja ndi kuno.

Place your Order

Kodi muli ndi zinthunzi Za ukwati wanu, birthday kapena  zochitika zilizonse zopadera zomwe mumafuna kumakumbukilabe nku...
31/07/2026

Kodi muli ndi zinthunzi Za ukwati wanu, birthday kapena zochitika zilizonse zopadera zomwe mumafuna kumakumbukilabe nkumaziona nyumba mwanu?

Ife Timapanga ma potrait Owala komanso a quality yapamwamba kwambiri.

Titumizilen ma order anu.

Whatsapp kapena kuimba phone : 0994 93 66 00

Free deliver mu Blantyre muno.

Timatumizanso kulikonse kudzera pa cts or speed courier or post office.

CANVAS POTRAIT PRICES:

# A4 ( MK 15,000)
# A3 ( MK 20,000)
# A2 ( MK 30,000)
# A1 ( MK 45,000)
# A0 ( MK 65,000)

Did you know you can get your portrait done with us at an affordable price?Surprise your special someone with a beautifu...
24/07/2026

Did you know you can get your portrait done with us at an affordable price?

Surprise your special someone with a beautiful portrait by us.

Portrait Prices:

• A0 (84 × 118 cm) – K65,000
• A1 (59 × 84 cm) – K45,000
• A2 (42 × 59 cm) – K30,000
• A3 (29 × 42 cm) – K20,000
• A4 (21 × 29 cm) – K15,000

Free delivery within Blantyre.
We also deliver to anywhere in Malawi.
Contact us or WhatsApp: 0994 93 66 00

Looking for Glass Frame Portraits?We create elegant, high-quality glass portraits at affordable prices.GLASS FRAME PRICE...
20/07/2026

Looking for Glass Frame Portraits?

We create elegant, high-quality glass portraits at affordable prices.

GLASS FRAME PRICES

A4 ( 21× 29 CM) MK 35,000
A3 ( 29 × 42 CM) MK 50,000
A2 ( 42 × 59 CM) MK 80,000

Location: Manja, Blantyre

Order with Us !!!!!!

Call Or Whatsapp: 0994 93 66 00

Kodi mukufuna wall portrait? Kapena muli ndi anzanu kapena abale omwe mukufuna kuwapangira? Ife timapanga ma wall portra...
20/07/2026

Kodi mukufuna wall portrait? Kapena muli ndi anzanu kapena abale omwe mukufuna kuwapangira?
Ife timapanga ma wall portrait okongola, apamwamba, komanso pa mtengo wabwino.

Mitengo Yama Potrait :

• A0 (84 × 118 cm) – MK65,000
• A1 (59 × 84 cm) – MK45,000
• A2 (42 × 59 cm) – MK30,000
• A3 (29 × 42 cm) – MK20,000
• A4 (21 × 29 cm) – MK15,000

Free delivery around Blantyre.

Timatumizanso kulikonse Malawi muno kudzera pa CTS,Speed,Post office or Direct minbus.

Contact us or WhatsApp: 0994 93 66 00

Timapanga ma Canvas Potrait A QUALITY komanso pa Mtengo omverera.Tikupezeka Ku Blantyre ku Manja pafupi ndi Chipiku Stor...
10/07/2026

Timapanga ma Canvas Potrait A QUALITY komanso pa Mtengo omverera.

Tikupezeka Ku Blantyre ku Manja pafupi ndi Chipiku Stores.

OUR PRICES :

• A0 (84 × 118 cm) – MK65,000
• A1 (59 × 84 cm) – MK45,000
• A2 (42 × 59 cm) – MK30,000
• A3 (29 × 42 cm) – MK20,000
• A4 (21 × 29 cm) – MK15,000

FREE delivery around Blantyre.

Timatumizanso kulikonse Malawi muno kudzera pa CTS Courier ,Speed Courier ,Post office or Direct minbus.

Contact us or WhatsApp: 0994 93 66 00

Pangitsani ma Wall Potrait Okongola komanso otsika Mtengo.Tikupezeka Ku Blantyre ku Manja pafupi ndi Chipiku Stores.Mite...
04/07/2026

Pangitsani ma Wall Potrait Okongola komanso otsika Mtengo.

Tikupezeka Ku Blantyre ku Manja pafupi ndi Chipiku Stores.

Mitengo Yama Potrait :

• A0 (84 × 118 cm) – K65,000
• A1 (59 × 84 cm) – K 45,000
• A2 (42 × 59 cm) – K 30,000
• A3 (29 × 42 cm) – K 20,000
• A4 (21 × 29 cm) – K 15,000

Free delivery around Blantyre.

Timatumizanso kulikonse Malawi muno kudzera pa CTS,Speed,Post office or Direct minbus.

Contact us or WhatsApp: 0994 93 66 00

Pangitsani ma Wall Potrait Okongola komanso a quality yabwino pa mtengoso wabwino.Tikupezeka Ku Blantyre ku Manja pafupi...
23/06/2026

Pangitsani ma Wall Potrait Okongola komanso a quality yabwino pa mtengoso wabwino.

Tikupezeka Ku Blantyre ku Manja pafupi ndi Chipiku Stores.

Mitengo Yama Potrait :

• A0 (84 × 118 cm) – MK65,000
• A1 (59 × 84 cm) – MK45,000
• A2 (42 × 59 cm) – MK30,000
• A3 (29 × 42 cm) – MK20,000
• A4 (21 × 29 cm) – MK15,000

Free delivery around Blantyre.

Timatumizanso kulikonse Malawi muno kudzera pa CTS,Speed,Post office or Direct minbus.

Contact us or WhatsApp: 0994 93 66 00

Did you know you can get your Canvas portrait done with us at an affordable price?Surprise your special someone with a b...
15/06/2026

Did you know you can get your Canvas portrait done with us at an affordable price?

Surprise your special someone with a beautiful portrait by us.

Canvas Portrait Prices:

• A0 (84 × 118 cm) – MK 65,000
• A1 (59 × 84 cm) – MK 45,000
• A2 (42 × 59 cm) –MK 30,000
• A3 (29 × 42 cm) – MK 20,000
• A4 (21 × 29 cm) – MK 15,000

Free delivery within Blantyre.
We also deliver to anywhere in Malawi through CTS, Speed Courier,Post Office and Direct Minibus .
Contact us or WhatsApp: 0994 93 66 00

Ma Canvas okongola kwambiri.✅ K25,000 pa Canvas imodzi✅ Set ya ma Canvas 3 — K70,000 yokhaKongoletsani nyumba kapena ofe...
08/06/2026

Ma Canvas okongola kwambiri.

✅ K25,000 pa Canvas imodzi

✅ Set ya ma Canvas 3 — K70,000 yokha

Kongoletsani nyumba kapena ofesi yanu ndi ma Canvas athu a quality yabwino komanso okongola.

📩 Inbox kapena WhatsApp kuti mu-ode lero
0994 93 66 00

Address

Manja
Blantyre
222

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Arclight Branding & Prints posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share