BLESS DANGER NIYABINGGY

BLESS DANGER NIYABINGGY Malawi's Afro-Dancehall artist, Graphic Designer & Content Creator. Currently based in Blantyre, Malawi


[email protected]
(2)

Ghetto Soche me here👐🙏Wagulu Network Entertainment
31/08/2026

Ghetto Soche me here👐🙏
Wagulu Network Entertainment



New music soon - Amayi🚨Real vibe
25/08/2026

New music soon - Amayi🚨
Real vibe

With my bro Yard Siny MWKwacha bho kuno🔥🔥
24/08/2026

With my bro Yard Siny MW
Kwacha bho kuno🔥🔥



Bless Danger - Sorry 🚨
21/08/2026

Bless Danger - Sorry 🚨





An apology song, Written and composed by Bless Danger, Audio prod b...

Enanu mumasiya munthu amene akukukondani kwambiri, ndikumakakamiza zinthu penapake.Bwanji kumakakamiza chikondi kwa munt...
14/08/2026

Enanu mumasiya munthu amene akukukondani kwambiri, ndikumakakamiza zinthu penapake.

Bwanji kumakakamiza chikondi kwa munthu
Amene tamuzindikila kuti akutikonda kwambiri?

Chifukwa ndizosowa kumudziwa munthu amene amakukonda kuchokera pansi pamtima, nde enafe Kaya kumakhala kulodzedwa...
Timakalimbana ndi munthu amene sitikudziwa kuti akutikonda ndi zolinga.
Kusiya munthu amene amatikonda popanda chifukwa.

Nde mukamakhala muziziwa kuti,
Sizabwino zonse zimene timazipeza kawiri.
Zina zikapita zimakhala zapita. Anthu amene mumawapanga chipongwewa, amene mumawasiya asanalakwe chifukwa choti mukulephera kuzindikila ubwino wawowa,

Tsiku linalake mudzawalakalaka
Koma idzakhala nthawi yatha.
Ndipo simudzapezaso munthu wabwino ndi mtima womwe ngati ameneyo.
Mapeto ake tizangopeza okuti adzingoimilira ngati thobwa lapamwamba
Koma opanda chikondi 😅🙏🏻

Samalani Zomwe MuliNazo, Chikondi Chenicheni Ndichosowa🙏
Follow me for more

Thank you 2,000 Facebook followers 🔥New music soon 🔥🇲🇼🚨
10/08/2026

Thank you 2,000 Facebook followers 🔥
New music soon 🔥🇲🇼🚨



Omwe tinasiidwa mwa chipongwe km pano tinaupeza mtendere let's gather here 😂🔥🙌
08/08/2026

Omwe tinasiidwa mwa chipongwe km pano tinaupeza mtendere let's gather here 😂🔥🙌



Throw back Thursday 🔥🤠
06/08/2026

Throw back Thursday 🔥🤠



Friday morning 8:00am🚨Tikumane pompano 🔥
05/08/2026

Friday morning 8:00am🚨
Tikumane pompano 🔥



Address

Chirimba
Blantyre

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when BLESS DANGER NIYABINGGY posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share